CHINYANJA: Bwana nkubwa watsopano wa bungwe lothana ndi katangale ku Malawi la Anti -Corruption Bureau ACB Martha Chizuma wati ali okondwa posankhidwa pa udindowu ngati mzimayi oyamba ndipo wati agwila ntchito motsata malamulo.

ENGLISH: The new Director of the Anti-Corruption Bureau in Malawi, Martha Chizuma, has expressed gratitude on the new role and will work in accordance with the law.